CHUMA CHOPEZEKA M’MAWU A MULUNGU
N’chifukwa Chiyani Kudzichepetsa N’kwabwino?
Yosiya anali wofunitsitsa kusangalatsa Yehova (2Mf 22:1-5)
Iye anavomereza zolakwa za anthu ake modzichepetsa (2Mf 22:13; w00-CN 9/15 29-30)
Chifukwa choti Yosiya anali wodzichepetsa, Yehova anamudalitsa (2Mf 22:18-20; w00-CN 9/15 30:2)
Yehova amasangalala nafe ngati modzichepetsa timamupempha kuti atitsogolere komanso timavomereza zomwe talakwitsa n’kukonza zolakwikazo.—Yak 4:6.