Genesis 16:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Chimenechi ndicho chifukwa chake chitsimecho chinatchedwa Beere-lahai-roi,*+ ndipo chili pakati pa Kadesi ndi Beredi. Genesis 25:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Abulahamu atamwalira, Mulungu anapitiriza kudalitsa Isaki mwana wake.+ Isakiyo anali kukhala pafupi ndi Beere-lahai-roi.+
14 Chimenechi ndicho chifukwa chake chitsimecho chinatchedwa Beere-lahai-roi,*+ ndipo chili pakati pa Kadesi ndi Beredi.
11 Abulahamu atamwalira, Mulungu anapitiriza kudalitsa Isaki mwana wake.+ Isakiyo anali kukhala pafupi ndi Beere-lahai-roi.+