Genesis 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+ Mateyu 1:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Abulahamu anabereka Isaki.+Isaki anabereka Yakobo.+Yakobo anabereka Yuda+ ndi abale ake.
2 Mulungu anapitiriza kuti: “Tenga Isaki+ mwana wako mmodzi yekhayo, mwana wako amene umamukonda kwambiriyo,+ ndipo muyende ulendo wopita ku Moriya.+ Kumeneko ukamupereke nsembe yopsereza paphiri limene ndidzakuuza.”+