Genesis 21:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Chotero Abulahamu anatcha mwana amene Sara anamuberekerayo dzina lakuti Isaki.+ 1 Mbiri 1:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ana a Abulahamu anali Isaki+ ndi Isimaeli.+ Luka 3:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 mwana wa Yakobo,+mwana wa Isaki,+mwana wa Abulahamu,+mwana wa Tera,+mwana wa Nahori,+