Genesis 27:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Tsopano Rabeka anauza mwana wake Yakobo+ kuti: “Ndamva bambo ako akuuza mkulu wako Esau kuti, Genesis 27:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Zitatha izi, Rabeka anali kuuza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Ndafika ponyansidwa nawo moyo wanga chifukwa cha ana aakazi achihetiwa.+ Ngati Yakobo atenga mkazi kuno pakati pa ana achiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+
46 Zitatha izi, Rabeka anali kuuza Isaki nthawi ndi nthawi kuti: “Ndafika ponyansidwa nawo moyo wanga chifukwa cha ana aakazi achihetiwa.+ Ngati Yakobo atenga mkazi kuno pakati pa ana achiheti ngati amenewa, ndi bwino ndingofa!”+