Genesis 28:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Choncho, Isaki anaitana Yakobo ndipo anamudalitsa n’kumulamula kuti: “Usatenge mkazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+ 2 Akorinto 6:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+
28 Choncho, Isaki anaitana Yakobo ndipo anamudalitsa n’kumulamula kuti: “Usatenge mkazi pakati pa ana aakazi a ku Kanani.+
14 Musamangidwe m’goli ndi osakhulupirira, chifukwa ndinu osiyana.+ Pali ubale wotani pakati pa chilungamo ndi kusamvera malamulo?+ Kapena pali kugwirizana kotani pakati pa kuwala ndi mdima?+