Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 31:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Ndiyeno Yakobo anaitanitsa Rakele ndi Leya, kuti abwere kubusa kumene iye anali ndi nkhosa zake.

  • Genesis 46:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Ana a Rakele,+ mkazi wa Yakobo, anali Yosefe+ ndi Benjamini.+

  • Rute 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pamenepo anthu onse ndi akulu amene anali pachipata anayankha kuti: “Ndife mboni! Yehova adalitse mkazi amene akulowa m’nyumba mwako kuti akhale ngati Rakele+ ndi Leya,+ akazi amene anabereka ana a nyumba ya Isiraeli.+ Uonetse kulemekezeka kwako mu Efurata+ ndi kudzipangira dzina m’Betelehemu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena