Genesis 35:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+ Genesis 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Kunena za ine, pamene ndinali kuchokera ku Padani,+ mayi ako Rakele anandifera+ panjira m’dziko la Kanani, patatsala mtunda ndithu kuti tifike ku Efurata. Zitatero, ndinawaika m’manda panjira yopita ku Efurata,+ kapena kuti Betelehemu.”+
19 Umu ndi mmene Rakele anamwalirira, ndipo anamuika m’manda ali m’njira popita ku Efurata, komwe ndi ku Betelehemu.+
7 Kunena za ine, pamene ndinali kuchokera ku Padani,+ mayi ako Rakele anandifera+ panjira m’dziko la Kanani, patatsala mtunda ndithu kuti tifike ku Efurata. Zitatero, ndinawaika m’manda panjira yopita ku Efurata,+ kapena kuti Betelehemu.”+