Oweruza 14:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Bambo ake anapitiriza ulendo wopita kwawo kwa mkazi uja, ndipo Samisoni anakonza phwando kumeneko,+ popeza umu ndi mmene achinyamata anali kuchitira. Mateyu 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ufumu wakumwamba uli ngati mfumu imene inakonza phwando la ukwati+ wa mwana wake. Chivumbulutso 19:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+
10 Bambo ake anapitiriza ulendo wopita kwawo kwa mkazi uja, ndipo Samisoni anakonza phwando kumeneko,+ popeza umu ndi mmene achinyamata anali kuchitira.
9 Mngeloyo anandiuza kuti: “Lemba: Odala ndiwo amene aitanidwa+ ku phwando la chakudya chamadzulo la ukwati+ wa Mwanawankhosa.” Anandiuzanso kuti: “Awa ndi mawu oona a Mulungu.”+