Genesis 31:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Potsirizira pake Yehova anauza Yakobo kuti: “Tsopano bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzakhalabe nawe.”+ Genesis 32:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki,+ inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu, kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+ Salimo 45:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+
3 Potsirizira pake Yehova anauza Yakobo kuti: “Tsopano bwerera kudziko la makolo ako ndi kwa abale ako,+ ndipo ine ndidzakhalabe nawe.”+
9 Atatero, Yakobo anati: “Mulungu wa kholo langa Abulahamu, Mulungu wa bambo anga Isaki,+ inu Yehova munandiuza kuti, ‘Bwerera kudziko lakwanu, kwa abale ako, ndipo ndidzakusamalira.’+
10 Iwe mwana wanga wamkazi, mvetsera ndipo ona ndi kutchera khutu.Uiwale anthu ako ndi nyumba ya bambo ako.+