Ekisodo 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+ Yobu 21:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Iwo amafuula nthawi zonse poimba maseche ndi azeze.+Amakhala akusangalala poimba zitoliro. Salimo 149:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Atamande dzina lake mwa kuvina.+Amuimbire nyimbo zomutamanda ndi maseche ndi zeze,+
20 Kenako Miriamu, mneneri wamkazi, mlongo wake wa Aroni,+ anatenga maseche m’manja mwake,+ ndipo akazi ena onse anam’tsatira akuimba maseche ndi kuvina.+