Ekisodo 22:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ngati wakubayo sanapezeke, azibweretsa mwininyumbayo pafupi ndi Mulungu woona*+ pofuna kuona ngati iyeyo sanatenge katundu wa mnzakeyo.
8 Ngati wakubayo sanapezeke, azibweretsa mwininyumbayo pafupi ndi Mulungu woona*+ pofuna kuona ngati iyeyo sanatenge katundu wa mnzakeyo.