Deuteronomo 16:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama. Deuteronomo 19:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 anthu awiri otsutsanawo aziima pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza amene aziweruza masiku amenewo.+ Salimo 82:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 82 Mulungu waima pakati pa msonkhano wake,+Ndipo akuweruza pakati pa milungu kuti:+
18 “Mudziikire oweruza+ ndi atsogoleri+ m’mizinda yanu yonse imene Yehova Mulungu wanu akukupatsani, malinga ndi mafuko anu. Oweruza ndi atsogoleriwo aziweruza anthu ndi chiweruzo cholungama.
17 anthu awiri otsutsanawo aziima pamaso pa Yehova, pamaso pa ansembe ndi oweruza amene aziweruza masiku amenewo.+