Numeri 11:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe. 1 Mbiri 23:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakati pawo panali oyang’anira ntchito ya panyumba ya Yehova okwana 24,000. Akapitawo+ ndi oweruza+ analipo 6,000.
16 Ndiyeno Yehova anauza Mose kuti: “Undisonkhanitsire akulu 70 mwa akulu a Isiraeli,+ amene ukuwadziwa kuti ndiwo akulu ndi oyang’anira pakati pa anthuwo.+ Upite nawo kuchihema chokumanako, ndipo akaime kumeneko limodzi nawe.
4 Pakati pawo panali oyang’anira ntchito ya panyumba ya Yehova okwana 24,000. Akapitawo+ ndi oweruza+ analipo 6,000.