Ekisodo 18:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Motero iwo anali kuweruza anthuwo pa nkhani iliyonse yoyenera. Nkhani yovuta anali kupita nayo kwa Mose,+ koma nkhani iliyonse yaing’ono, iwo monga oweruza anali kuisamalira. Deuteronomo 1:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+ 2 Mbiri 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Anaika oweruza m’dziko lonselo, mumzinda ndi mzinda, m’mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+
26 Motero iwo anali kuweruza anthuwo pa nkhani iliyonse yoyenera. Nkhani yovuta anali kupita nayo kwa Mose,+ koma nkhani iliyonse yaing’ono, iwo monga oweruza anali kuisamalira.
16 “Pa nthawi imeneyo ndinalamula oweruza anu kuti, ‘Mukamazenga mlandu wa pakati pa abale anu, muziweruza mwachilungamo+ pakati pa munthu ndi m’bale wake, kapena ndi mlendo wokhala m’nyumba mwake.+
5 Anaika oweruza m’dziko lonselo, mumzinda ndi mzinda, m’mizinda yonse ya Yuda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri.+