Yoswa 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Miyala imeneyo idzakhala chizindikiro pakati panu.+ Ana anu akamadzafunsa m’tsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+
6 Miyala imeneyo idzakhala chizindikiro pakati panu.+ Ana anu akamadzafunsa m’tsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+