Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Ndiyeno ana anu akadzakufunsani kuti, ‘Kodi mwambo umenewu umatanthauza chiyani?’+

  • Ekisodo 13:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 “Ndiyeno m’tsogolo, mwana wanu akadzakufunsani+ kuti, ‘Kodi zimenezi zikutanthauza chiyani?’ Mudzamuyankhe kuti, ‘Yehova anatitulutsa ndi mphamvu ya dzanja lake mu Iguputo,+ m’nyumba ya ukapolo.+

  • Deuteronomo 6:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 “Mwana wako akadzakufunsa tsiku lina m’tsogolo+ kuti, ‘Kodi zikumbutso, malangizo ndi zigamulo izi zimene Yehova Mulungu wathu anakupatsani, zimatanthauza chiyani?’

  • Yoswa 4:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Kenako anauza ana a Isiraeli kuti: “Ana anu akamadzafunsa abambo awo m’tsogolomu kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+

  • Salimo 78:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  3 Amene tinamva ndipo tikuwadziwa,+

      Komanso amene makolo athu anatifotokozera.+

  • Yesaya 38:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Munthu wamoyo, amene akupuma, ndi amene angakutamandeni,+

      Ngati mmene ineyo ndikuchitira lero.+

      Bambo akhoza kuphunzitsa+ ana ake za kukhulupirika kwanu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena