Yoswa 4:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Miyala imeneyo idzakhala chizindikiro pakati panu.+ Ana anu akamadzafunsa m’tsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+ Salimo 44:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+M’masiku akale.+
6 Miyala imeneyo idzakhala chizindikiro pakati panu.+ Ana anu akamadzafunsa m’tsogolo muno kuti, ‘Kodi miyalayi ndi ya chiyani?’+
44 Inu Mulungu, ife tamva ndi makutu athu,Makolo athu anatifotokozera+Ntchito zimene inu munachita m’masiku awo,+M’masiku akale.+