Genesis 25:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+ Genesis 28:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero Esau anapita kwa Isimaeli* n’kukatengako mkazi kuwonjezera pa akazi amene anali nawo.+ Mkaziyo dzina lake anali Mahalati, ndipo anali mlongo wake wa Nebayoti. Mahalati anali mwana wa Isimaeli, mwana wa Abulahamu.
13 Awa ndiwo mayina a ana a Isimaeli, amene kunachokera mabanja awo: Nebayoti,+ mwana woyamba wa Isimaeli, Kedara,+ Adibeele, Mibisamu,+
9 Chotero Esau anapita kwa Isimaeli* n’kukatengako mkazi kuwonjezera pa akazi amene anali nawo.+ Mkaziyo dzina lake anali Mahalati, ndipo anali mlongo wake wa Nebayoti. Mahalati anali mwana wa Isimaeli, mwana wa Abulahamu.