Genesis 27:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+ Genesis 32:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+
39 Koma Isaki bambo ake anamuuza kuti: “Taona, udzakhala kutali ndi nthaka yachonde, kotalikirana ndi mame akumwamba.+
3 Kenako Yakobo anatsogoza amithenga+ ake powatumiza kwa Esau m’bale wake, kudziko la Seiri,+ kudera la Edomu.+