Rute 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+ Mateyu 22:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Mphunzitsi, Mose anati, ‘Ngati munthu wamwalira wopanda ana, m’bale wake ayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana.’+
13 kodi mungawadikirirebe mpaka atakula? Kodi mungadzisungebe osakwatiwa powadikirira? Ayi ndithu ana anga, zimene zinakuchitikirani zimandiwawa kwambiri, pakuti dzanja la Yehova landiukira.”+
24 “Mphunzitsi, Mose anati, ‘Ngati munthu wamwalira wopanda ana, m’bale wake ayenera kukwatira mkazi wamasiyeyo ndi kuberekera m’bale wake uja ana.’+