Levitiko 22:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Koma mwana wa wansembe akakhala mkazi wamasiye, kapena wosiyidwa ukwati alibe mwana aliyense, ndipo wabwerera kunyumba kwa bambo ake kumene anali ali mwana,+ angadye nawo chakudya cha bambo ake.+ Koma munthu wamba asadye nawo chakudya chimenecho.
13 Koma mwana wa wansembe akakhala mkazi wamasiye, kapena wosiyidwa ukwati alibe mwana aliyense, ndipo wabwerera kunyumba kwa bambo ake kumene anali ali mwana,+ angadye nawo chakudya cha bambo ake.+ Koma munthu wamba asadye nawo chakudya chimenecho.