Salimo 105:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+ Machitidwe 7:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+
17 Mulungu anatsogoza munthu kuti anthu akewo abwere pambuyo pake,Anatumiza Yosefe amene anagulitsidwa kuti akhale kapolo.+
9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+