Machitidwe 7:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 ndipo anamulanditsa m’masautso ake onse. Anamupatsanso chisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Ndipo anamuika kuti ayang’anire Iguputo ndi nyumba yonse ya Farao.+
10 ndipo anamulanditsa m’masautso ake onse. Anamupatsanso chisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Ndipo anamuika kuti ayang’anire Iguputo ndi nyumba yonse ya Farao.+