Genesis 41:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako ndinaonanso ng’ombe zina 7 zikutuluka mumtsinjewo pambuyo pa zoyamba zija. Ng’ombe zimenezi zinali zamaonekedwe onyansa ndi zowonda.+ Sindinaonepo ng’ombe zonyansa ngati zimenezo m’dziko lonse la Iguputo.
19 Kenako ndinaonanso ng’ombe zina 7 zikutuluka mumtsinjewo pambuyo pa zoyamba zija. Ng’ombe zimenezi zinali zamaonekedwe onyansa ndi zowonda.+ Sindinaonepo ng’ombe zonyansa ngati zimenezo m’dziko lonse la Iguputo.