Genesis 41:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Anaonanso ng’ombe zina 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailowo pambuyo pa zoyambazo. Zimenezi zinali zonyansa ndi zowonda,+ ndipo zinaima pambali pa zinazo m’mbali mwa mtsinjemo.
3 Anaonanso ng’ombe zina 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailowo pambuyo pa zoyambazo. Zimenezi zinali zonyansa ndi zowonda,+ ndipo zinaima pambali pa zinazo m’mbali mwa mtsinjemo.