Genesis 39:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Tsopano Yosefe uja, Aisimaeli+ anapita naye ku Iguputo,+ ndipo kumeneko anakam’gulitsa kwa Potifara.+ Potifara anali Mwiguputo, yemwe anali nduna ya panyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu.
39 Tsopano Yosefe uja, Aisimaeli+ anapita naye ku Iguputo,+ ndipo kumeneko anakam’gulitsa kwa Potifara.+ Potifara anali Mwiguputo, yemwe anali nduna ya panyumba ya Farao, komanso mkulu wa asilikali olondera mfumu.