Genesis 40:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Kuti ndipezeke kuno anachita chondiba kudziko la Aheberi,+ ndiponso kuno palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire m’ndende muno.”+ Danieli 2:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”
15 Kuti ndipezeke kuno anachita chondiba kudziko la Aheberi,+ ndiponso kuno palibe chilichonse chimene ndinalakwa choti andiikire m’ndende muno.”+
25 Mofulumira, Arioki anapititsa Danieli kwa mfumu ndi kuiuza kuti: “Ndapeza mwamuna wamphamvu pakati pa anthu amene anatengedwa ukapolo+ ku Yuda yemwe angamasulire maloto anu mfumu.”