Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 39:8
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 8 Koma Yosefe anali kukana+ ndi kuuza mkazi wa mbuye wakeyo kuti: “Chifukwa cha ine, mbuye wanga sadera nkhawa za chilichonse m’nyumba muno, ndipo chilichonse chimene iye ali nacho wachipereka m’manja mwanga.+

  • Salimo 105:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Mawu a Yehova anamuyenga,+

      Kufikira pamene lonjezo la Mulungu linakwaniritsidwa.+

  • Salimo 119:86
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    •  86 Malamulo anu onse ndi odalirika.+

      Odzikuza andizunza popanda chifukwa. Chonde, ndithandizeni.+

  • Danieli 6:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Mulungu wanga+ watumiza mngelo wake+ kudzatseka pakamwa pa mikango.+ Chotero mikangoyo sinandivulaze, chifukwa iye sanandipeze ndi mlandu uliwonse+ ndiponso sindinakulakwireni chilichonse inu mfumu.”+

  • Yohane 15:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Zili choncho kuti mawu olembedwa m’Chilamulo akwaniritsidwe. Mawu ake ndi akuti, ‘Anadana nane popanda chifukwa.’+

  • Aheberi 12:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Zoonadi, palibe chilango chimene chimamveka chosangalatsa pa nthawi yomwe ukuchilandira, koma chimakhala chowawa.+ Komabe pambuyo pake, kwa anthu amene aphunzirapo kanthu pa chilangocho, chimabala chipatso chamtendere,+ chomwe ndi chilungamo.+

  • 1 Petulo 3:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Pakuti ndi bwino kuvutika chifukwa chochita zabwino,+ ngati Mulungu walola, kusiyana ndi kuvutika chifukwa chochita zoipa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena