Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Pambuyo pake, munthu wina amene anathawa anafika kwa Abulamu Mheberi.+ Pa nthawiyo n’kuti Abulamu akukhala m’hema wake pakati pa mitengo ikuluikulu. Mitengoyo mwiniwake anali Mamure, yemwe anali Muamori.+ Ameneyu anali m’bale wake wa Esikolo, ndipo analinso m’bale wake wa Aneri.+ Iwowa anapanga ubale ndi Abulamu.

  • Genesis 37:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Tsopano amuna amalonda achimidiyani+ aja anali kudutsa mumsewu. Pamenepo abale a Yosefe anamutulutsa m’chitsimemo+ n’kumugulitsa kwa Aisimaeliwo. Anamugulitsa ndalama zasiliva 20,+ ndipo iwo anapita naye ku Iguputo.

  • Genesis 41:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Tinalinso ndi mnyamata wina wachiheberi+ kumeneko. Iyeyo anali wantchito wa mkulu wa asilikali olondera mfumu.+ Titamufotokozera maloto athu,+ anatimasulira matanthauzo ake. Aliyense anam’masulira malinga ndi maloto amene analota.

  • Ekisodo 21:16
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 16 “Wakuba munthu+ ndi kum’gulitsa+ kapena munthu amene wapezeka ndi munthu wobedwayo, aziphedwa ndithu.+

  • Machitidwe 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena