Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Salimo 25:14
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 14 Ubwenzi wolimba ndi Yehova ndi wa anthu amene amamuopa,+

      Pangano lakenso ndi la anthu oterowo, ndipo iye amawadziwitsa panganolo.+

  • Danieli 5:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anachita zimenezi chifukwa munthuyu anali ndi luso lodabwitsa, anali wodziwa zinthu ndi wozindikira pa nkhani yomasulira maloto,+ kumasulira mikuluwiko ndi kumasula mfundo. Zinthu zonsezi zinapezeka mwa munthu ameneyu+ Danieli, amene mfumu inamupatsa dzina lakuti Belitesazara.+ Tsopano itanani Danieli kuti adzakuuzeni kumasulira kwa zolembedwazi.”

  • Machitidwe 7:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 ndipo anamulanditsa m’masautso ake onse. Anamupatsanso chisomo ndi nzeru pamaso pa Farao mfumu ya Iguputo. Ndipo anamuika kuti ayang’anire Iguputo ndi nyumba yonse ya Farao.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena