Genesis 41:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Kenako iye anaona ng’ombe 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailo. Ng’ombezo zinali zokongola m’maonekedwe ndi zonenepa, ndipo zinali kudya udzu wa m’mbali mwa mtsinjewo.+
2 Kenako iye anaona ng’ombe 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailo. Ng’ombezo zinali zokongola m’maonekedwe ndi zonenepa, ndipo zinali kudya udzu wa m’mbali mwa mtsinjewo.+