Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 1:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Kwa nyama iliyonse yam’tchire ya padziko lapansi, ndi kwa cholengedwa chilichonse chouluka m’mlengalenga, komanso kwa chokwawa chilichonse cha padziko lapansi chimene chili ndi moyo, ndapereka zomera zonse kuti zikhale chakudya chawo.”+ Ndipo zinaterodi.

  • Genesis 41:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Ndiyeno ndinaona ng’ombe 7 zikutuluka mumtsinje wa Nailo. Ng’ombezo zinali zonenepa ndi zooneka bwino, ndipo zinayamba kudya udzu wa m’mbali mwa mtsinjewo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena