Genesis 41:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Tsopano ng’ombe zonyansa ndi zowondazo zinayamba kudya ng’ombe 7 zooneka bwino ndi zonenepa zija.+ Kenako Farao anagalamuka.+
4 Tsopano ng’ombe zonyansa ndi zowondazo zinayamba kudya ng’ombe 7 zooneka bwino ndi zonenepa zija.+ Kenako Farao anagalamuka.+