Genesis 45:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya. Kwatsala zaka zisanu za njala,+ ndipo sindikufuna kuti inuyo ndi a m’nyumba yanu, ndi zonse zimene muli nazo muvutike ndi njala.”’ Genesis 47:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+
11 Kumeneko ndizidzakupatsani chakudya. Kwatsala zaka zisanu za njala,+ ndipo sindikufuna kuti inuyo ndi a m’nyumba yanu, ndi zonse zimene muli nazo muvutike ndi njala.”’
19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+