Genesis 47:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Kenako anauza Farao kuti: “Tabwera kuno kudzakhala monga alendo,+ chifukwa akapolo anufe tilibe chakudya chopatsa ziwetozi,+ popeza njala yafika poipa kwambiri ku Kanani.+ Ndiye chonde, tiloleni ife akapolo anu tikhale ku Goseni.”+ Salimo 33:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kuti apulumutse moyo wawo ku imfa,+Ndi kuwasunga ndi moyo pa nthawi ya njala.+
4 Kenako anauza Farao kuti: “Tabwera kuno kudzakhala monga alendo,+ chifukwa akapolo anufe tilibe chakudya chopatsa ziwetozi,+ popeza njala yafika poipa kwambiri ku Kanani.+ Ndiye chonde, tiloleni ife akapolo anu tikhale ku Goseni.”+