Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 15:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako Mulungu anauza Abulamu kuti: “Udziwe ndithu kuti mbewu yako idzakhala mlendo m’dziko la eni,+ ndipo idzatumikira eni dzikolo. Iwo adzasautsa mbewu yako kwa zaka 400.+

  • Deuteronomo 26:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo uzikanena pamaso pa Yehova Mulungu wako kuti, ‘Bambo anga anali Msiriya+ wotsala pang’ono kufa. Anapita ku Iguputo+ ndi anthu ochepa chabe+ a m’banja lake kukakhala kumeneko monga mlendo, koma anakhaladi mtundu waukulu ndi wamphamvu kumeneko.+

  • Salimo 105:23
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 23 Kenako Isiraeli anapita ku Iguputo,+

      Yakobo anakhala monga mlendo m’dziko la Hamu.+

  • Yesaya 52:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita ku Iguputo kuti akakhale ngati alendo.+ Ndiyeno Asuri anawapondereza popanda chifukwa.”

  • Machitidwe 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Ndipo Mulungu ananenanso kuti mbewu yake idzakhala alendo+ m’dziko lachilendo,+ ndipo anthu adzawasandutsa akapolo ndi kuwasautsa kwa zaka 400.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena