Genesis 42:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Tonsefe ndife ana a munthu mmodzi, ndipo ndife anthu achilungamo. Akapolo anufe sitichita zaukazitape ayi.”+ Miyambo 11:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+ Miyambo 14:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Munthu woyenda mowongoka mtima amaopa Yehova,+ koma munthu amene amayenda m’njira zokhotakhota amanyoza Mulungu.+
11 Tonsefe ndife ana a munthu mmodzi, ndipo ndife anthu achilungamo. Akapolo anufe sitichita zaukazitape ayi.”+
6 Kulungama kwa anthu owongoka mtima n’kumene kudzawapulumutse,+ koma anthu ochita zinthu mwachinyengo adzagwidwa ndi zolakalaka zawo.+
2 Munthu woyenda mowongoka mtima amaopa Yehova,+ koma munthu amene amayenda m’njira zokhotakhota amanyoza Mulungu.+