Genesis 42:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamenepo iwo anati: “Akapolo anufe tilipo 12 pa ubale wathu.+ Ndife ana a munthu mmodzi amene akukhala ku Kanani.+ Wamng’ono kwambiri watsala ndi bambo athu,+ koma winayo kulibenso.”+
13 Pamenepo iwo anati: “Akapolo anufe tilipo 12 pa ubale wathu.+ Ndife ana a munthu mmodzi amene akukhala ku Kanani.+ Wamng’ono kwambiri watsala ndi bambo athu,+ koma winayo kulibenso.”+