Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 37:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 Tiyeni timugulitse kwa Aisimaeliwa,+ tisam’pweteke ayi.+ Ndipotu ndi m’bale wathu ameneyu, magazi* athu enieni.” Atamva mawuwa, iwo anamvera m’bale wawoyo.+

  • Genesis 37:35
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 35 Ana ake onse aamuna ndi aakazi anali kupita kukam’tonthoza,+ koma iye anali kukana kutonthozedwa. Anali kunena kuti:+ “Ayi! Ndidzalira mpaka kutsikira ku Manda* kumene kuli mwana wanga.” Ndipo bambo akewo anapitiriza kumulira.

  • Genesis 44:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ife tinakuyankhani mbuyanga kuti, ‘Bambo tili nawo koma ndi okalamba. Ali ndi mwana amene anabereka atakalamba, amene ndiye wamng’ono pa ife tonse.+ M’bale wake wa mimba imodzi anamwalira, moti anatsala yekha,+ ndipo bambo amam’konda kwambiri.’

  • Genesis 45:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Atafika, anauza bambo awo kuti: “Yosefe uja ali moyo! Ndiye woyang’anira dziko lonse la Iguputo!”+ Yakobo atamva zimenezo sizinam’khudze chifukwa sanazikhulupirire.+

  • Machitidwe 7:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Mitu ya mabanja ija inachitira nsanje+ Yosefe ndi kumugulitsa ku Iguputo.+ Koma Mulungu anali naye,+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena