Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 35:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+

  • Genesis 42:38
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 38 Komabe bambo awo anati: “Zoti mwana wanga apite nanu, izo ndakana, chifukwa m’bale wake anafa, ndipo iye anatsala yekha.+ Ngati angakumane ndi tsoka n’kufa panjira, ndithu mudzatsitsira ku Manda+ imvi zanga ndi chisoni.”

  • Genesis 43:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Koma iwo anayankha kuti: “Munthuyo anachita kufunsa za ife ndi banja lathu kuti, ‘Kodi bambo anu akali ndi moyo?+ Kodi muli ndi m’bale wanu wina?’ Ndipo ife tinayankha mogwirizana ndi zimene anafunsa.+ Nanga tikanadziwa bwanji zoti anena kuti, ‘Mukam’bweretse kuno m’bale wanuyo’?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena