Genesis 35:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+ Genesis 42:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Koma Yakobo sanalole kuti Benjamini,+ m’bale wake wa Yosefe, apite limodzi ndi abale akewo, chifukwa anati: “Mwina angakumane ndi tsoka n’kufa.”+
18 Pomalizira pake, pamene moyo wake+ unali kutayika (pakuti anamwalira),+ anatcha mwanayo dzina lakuti Beni-oni.* Koma bambo ake anamutcha Benjamini.*+
4 Koma Yakobo sanalole kuti Benjamini,+ m’bale wake wa Yosefe, apite limodzi ndi abale akewo, chifukwa anati: “Mwina angakumane ndi tsoka n’kufa.”+