Genesis 42:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Chabwino, ndikuyesani motere kuti ndione ngati mukunena zoona: Simuchoka kuno mpaka mng’ono wanuyo atabwera,+ ndithu pali Farao wamoyo!
15 Chabwino, ndikuyesani motere kuti ndione ngati mukunena zoona: Simuchoka kuno mpaka mng’ono wanuyo atabwera,+ ndithu pali Farao wamoyo!