-
Genesis 42:35Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
35 Tsopano pamene anali kukhuthula matumba awo, aliyense anapeza mpukutu wa ndalama zake m’thumba lake. Ataziona ndalamazo limodzi ndi bambo awo, onse anachita mantha.
-