Numeri 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Paja kale makolo athu anapita ku Iguputo,+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.+ Aiguputowo anatizunza ife ndi makolo athu.+ Salimo 105:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Kenako Isiraeli anapita ku Iguputo,+Yakobo anakhala monga mlendo m’dziko la Hamu.+ Yesaya 52:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita ku Iguputo kuti akakhale ngati alendo.+ Ndiyeno Asuri anawapondereza popanda chifukwa.” Machitidwe 7:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Yakobo anapita ku Iguputo+ kumene iye ndi makolo athu+ aja anamwalirira.+
15 Paja kale makolo athu anapita ku Iguputo,+ ndipo tinakhala kumeneko zaka zambiri.+ Aiguputowo anatizunza ife ndi makolo athu.+
4 Pakuti Yehova, Ambuye Wamkulu Koposa, wanena kuti: “Poyamba anthu anga anapita ku Iguputo kuti akakhale ngati alendo.+ Ndiyeno Asuri anawapondereza popanda chifukwa.”