Hagai 2:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+ Luka 6:44 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+ Yakobo 3:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Abale anga, kodi mkuyu ungabale maolivi, kapena mtengo wa mpesa ungabale nkhuyu?+ Ngakhale madzi amchere sangatulutse madzi abwino.
19 Kodi mbewu zilipobe m’dzenje losungiramo mbewu?+ Kodi mitengo ya mpesa, mitengo ya mkuyu, mitengo ya makangaza* ndi mitengo ya maolivi ikuberekabe zipatso? Kuyambira lero ndikupatsani madalitso.’”+
44 Pakuti mtengo uliwonse umadziwika ndi chipatso chake.+ Mwachitsanzo, anthu sathyola nkhuyu mumtengo waminga, kapena kudula mphesa m’chitsamba chaminga.+
12 Abale anga, kodi mkuyu ungabale maolivi, kapena mtengo wa mpesa ungabale nkhuyu?+ Ngakhale madzi amchere sangatulutse madzi abwino.