Genesis 41:43 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 43 Ndiponso, anamukweza pagaleta* lachiwiri laulemu limene anali nalo,+ ndipo anthu anali kufuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* posonyeza kuti ndi wamkulu m’dziko lonse la Iguputo.
43 Ndiponso, anamukweza pagaleta* lachiwiri laulemu limene anali nalo,+ ndipo anthu anali kufuula patsogolo pake kuti, “A·vrékh!”* posonyeza kuti ndi wamkulu m’dziko lonse la Iguputo.