Genesis 47:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+ Miyambo 14:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wonyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,+ koma wodala ndi munthu wokomera mtima anthu osautsika.+
19 Tiferenji ife inu mukuona,+ ndipo minda yathu ikhalirenji yogonera? Mutigule limodzi ndi minda yathu potipatsa chakudya+ kuti tikhale akapolo a Farao. Mutipatse tirigu kuti tikhale ndi moyo tisafe, kutinso minda yathu isagonere.”+
21 Munthu wonyoza mnzake ndiye kuti akuchimwa,+ koma wodala ndi munthu wokomera mtima anthu osautsika.+