Genesis 47:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Nthaka ya ansembe+ yokha ndi imene sanaigule, chifukwa chakudya chimene ansembe anali kudya chinali kuchokera kwa Farao.+ N’chifukwa chake ansembewo sanagulitse nthaka yawo.+
22 Nthaka ya ansembe+ yokha ndi imene sanaigule, chifukwa chakudya chimene ansembe anali kudya chinali kuchokera kwa Farao.+ N’chifukwa chake ansembewo sanagulitse nthaka yawo.+