Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Nehemiya 13:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Ndiyeno ndinaika Selemiya wansembe, Zadoki wokopera Malemba ndi Pedaya mmodzi mwa Alevi, kuti akhale oyang’anira malo osungira zinthu. Amenewa anali kuyang’anira Hanani mwana wa Zakuri amene anali mwana wa Mataniya,+ pakuti anthu anali kuwaona kuti ndi okhulupirika.+ Iwowa anapatsidwa udindo wogawa+ zinthu kwa abale awo.

  • Mateyu 10:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Musatenge thumba la chakudya cha pa ulendo, kapena malaya awiri amkati, nsapato kapena ndodo, chifukwa wantchito ayenera kulandira chakudya chake.+

  • 1 Akorinto 9:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kodi simukudziwa kuti anthu ochita ntchito zopatulika amadya+ za m’kachisi, ndipo amene amatumikira+ kuguwa lansembe nthawi zonse amagawana gawo ndi guwa lansembe?

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena